Oweruza 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone. Oweruza 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zitatero, Gidiyoni anagwidwa ndi mzimu wa Yehova,+ moti analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndipo Aabi-ezeri+ anasonkhana pamodzi nʼkuyamba kumutsatira.
11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone.
34 Zitatero, Gidiyoni anagwidwa ndi mzimu wa Yehova,+ moti analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndipo Aabi-ezeri+ anasonkhana pamodzi nʼkuyamba kumutsatira.