Deuteronomo 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 ‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti aphe munthu wosalakwa.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
25 ‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti aphe munthu wosalakwa.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)