Luka 12:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akapita nanu kumabwalo amilandu,* kwa akuluakulu aboma komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani,+ 12 chifukwa mzimu woyera udzakuphunzitsani mu ola lomwelo zimene mukuyenera kunena.”+
11 Akapita nanu kumabwalo amilandu,* kwa akuluakulu aboma komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani,+ 12 chifukwa mzimu woyera udzakuphunzitsani mu ola lomwelo zimene mukuyenera kunena.”+