1 Atesalonika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano*+ komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate komanso Ambuye Yesu Khristu kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zikhale nanu. 1 Petulo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakulemberani kalata yachiduleyi kudzera mwa Silivano,*+ mʼbale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi kuti ndikulimbikitseni ndi kukutsimikizirani kuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu nʼkumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.
1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano*+ komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate komanso Ambuye Yesu Khristu kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zikhale nanu.
12 Ndakulemberani kalata yachiduleyi kudzera mwa Silivano,*+ mʼbale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi kuti ndikulimbikitseni ndi kukutsimikizirani kuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu nʼkumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.