Salimo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munamupatsa mphamvu kuti alamulire ntchito za manja anu.+Mwaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake: Aefeso 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+
22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+