Aefeso 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ mʼbale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika wa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+ Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine.
21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ mʼbale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika wa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+
7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine.