Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+Mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”+ Machitidwe 7:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma iye, atadzazidwa ndi mzimu woyera, anayangʼanitsitsa kumwamba ndipo anaona ulemerero wa Mulungu ndiponso Yesu ataima kudzanja lamanja la Mulungu.+ Aheberi 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo yothandiza mpaka kalekale, ndipo anakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+
110 Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+Mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”+
55 Koma iye, atadzazidwa ndi mzimu woyera, anayangʼanitsitsa kumwamba ndipo anaona ulemerero wa Mulungu ndiponso Yesu ataima kudzanja lamanja la Mulungu.+
12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo yothandiza mpaka kalekale, ndipo anakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+