Deuteronomo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Lamulo limene ndikukupatsani leroli si lovuta kwa inu kulitsatira, ndipo silili poti simungathe kulipeza.*+ Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
11 Lamulo limene ndikukupatsani leroli si lovuta kwa inu kulitsatira, ndipo silili poti simungathe kulipeza.*+
8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+