-
Afilipi 3:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma ife ndife nzika+ zakumwamba+ ndipo tikuyembekezera mwachidwi mpulumutsi wochokera kumeneko amene ndi Ambuye Yesu Khristu.+ 21 Iye adzasintha thupi lathu lonyozekali kuti lifanane* ndi thupi lake laulemerero.+ Adzachita zimenezi pogwiritsa ntchito mphamvu zake zazikulu zimene zimamuthandiza kugonjetsa zinthu zonse kuti zikhale pansi pake.+
-