Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 14
  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Mudzapeza Mphoto Chifukwa cha Ntchito Yanu”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Muzichita Zinthu Mwanzeru pa Nthawi Yomwe Zinthu Zikuyenda Bwino
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 14

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?

Asa anadalira Yehova kuti agonjetse gulu lalikulu la asilikali (2Mb 14:9-12; w21.03 5 ¶12)

Patapita nthawi Asa anadalira Asiriya kuti agonjetse gulu laling’ono la asilikali (2Mb 16:1-3; w21.03 5 ¶13)

Yehova sanasangalale ndi Asa chifukwa anasiya kumudalira (2Mb 16:7-9)

Zithunzi: 1. Wachinyamata akubatizidwa. 2. Wachinyamata yemweyo akusankha pulogalamu yoti aonere pa TV.

Tikhoza kudalira Yehova tikamapanga zosankha zikuluzikulu zimene zingasinthe moyo wathu, koma bwanji panthawi zina? M’pofunika kuti tizikumbukira Yehova m’njira zathu zonse.​—Miy 3:5, 6; w21.03 6 ¶14.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena