Numeri 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo anam’sunga kaye+ chifukwa panalibe lamulo lachindunji lonena chilango chimene akanapereka.