Deuteronomo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,7/1/1992, tsa. 17
16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+