Mlaliki 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndaonapo antchito atakwera pamahatchi,* koma akalonga akuyenda pansi ngati antchito.+