-
Yohane 12:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Chotero khamu la anthu amene anali ataimirira pamenepo ndi kumva zimenezi anayamba kunena kuti kwagunda bingu. Ena anayamba kunena kuti: “Mngelo walankhula naye.”
-