1 Atesalonika 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi abale, mukukumbukira ntchito+ yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu. Mwa kugwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza,+ tinalalikira uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu.
9 Ndithudi abale, mukukumbukira ntchito+ yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu. Mwa kugwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza,+ tinalalikira uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu.