1 Atesalonika 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiponso pamene tinali nanu limodzi, tinali kukuuziranitu+ kuti tiyenera kudzakumana ndi masautso,+ ndipo mmene zachitikiramu ndi mmenenso inu mukudziwira.+
4 Ndiponso pamene tinali nanu limodzi, tinali kukuuziranitu+ kuti tiyenera kudzakumana ndi masautso,+ ndipo mmene zachitikiramu ndi mmenenso inu mukudziwira.+