2 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuyambira panopa mpaka m’tsogolo, andisungira chisoti chachifumu chachilungamo.+ Ambuye, woweruza wolungama,+ adzandipatsa mphotoyo+ m’tsikulo.+ Sadzapatsa ine ndekha ayi, komanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 276-277
8 Kuyambira panopa mpaka m’tsogolo, andisungira chisoti chachifumu chachilungamo.+ Ambuye, woweruza wolungama,+ adzandipatsa mphotoyo+ m’tsikulo.+ Sadzapatsa ine ndekha ayi, komanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere.