Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 120:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo.

      Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+

  • Ezekieli 32:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kumeneko nʼkumene kuli Meseki ndi Tubala+ limodzi ndi magulu a anthu awo onse amene ankawatsatira. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu amene anabaidwa ndi lupanga chifukwa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani