-
Levitiko 26:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo. Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.*
-