-
Levitiko 8:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7, mpaka masiku okuikani kuti mukhale ansembe atatha, chifukwa padzatenga masiku 7 kuti muikidwe kukhala ansembe.+
-