-
Levitiko 11:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Aliyense amene angadye nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Aliyense amene anganyamule nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
-