-
Levitiko 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+
-
-
Numeri 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Aliyense wokhudza mtembo wa munthu aliyense, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7.+
-
-
Numeri 19:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chinthu chilichonse chimene munthu wodetsedwayo angakhudze, chizikhala chodetsedwa. Komanso munthu amene angakhudze chinthucho, azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.’”+
-