Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 25:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma ngati munthu amene anagulitsa malo sanapeze ndalama zoti angabwezere kwa amene anagulayo, malo amene anagulitsawo apitirizebe kukhala a munthu amene anawagulayo mpaka Chaka cha Ufulu chitafika.+ Mʼchaka chimenecho malowo azibwezedwa kwa mwiniwake ndipo amene anagulitsa maloyo azibwerera kumalo akewo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani