Ekisodo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+ Ezekieli 45:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita chikondwerero cha Pasika.+ Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda zofufumitsa.+ 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+
21 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita chikondwerero cha Pasika.+ Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda zofufumitsa.+