-
Numeri 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Upange malipenga awiri+ asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa msonkhano komanso posamutsa msasa.
-
-
Numeri 10:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ngati mukufunika kumenya nkhondo mʼdziko lanu polimbana ndi mdani amene akukuzunzani, muziliza malipengawo+ posonyeza kuti mukuitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Yehova Mulungu wanu adzakukumbukirani ndipo adzakupulumutsani kwa adani anuwo.
-