-
Numeri 3:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mabanja a Alibini+ ndi Asimeyi anachokera mwa Gerisoni. Amenewa ndi amene anali mabanja a Agerisoni.
-
-
Numeri 3:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mabanja a Agerisoni ankamanga misasa yawo kumbuyo kwa chihema,+ mbali yakumadzulo.
-