Oweruza 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mʼmutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri* wa Mulungu kuchokera tsiku limene adzabadwe.* Iye adzatsogolera populumutsa Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+ Oweruza 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Samueli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
5 Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mʼmutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri* wa Mulungu kuchokera tsiku limene adzabadwe.* Iye adzatsogolera populumutsa Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+