-
Levitiko 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+
-
-
Levitiko 21:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Iye asayandikire munthu aliyense wakufa+ ndipo asamadzidetse ngakhale amene wamwalirayo atakhala bambo ake kapena mayi ake.
-