-
Levitiko 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako Aroni anakweza manja ake nʼkuloza anthuwo ndipo anawadalitsa.+ Atatero anatsika kuguwa lansembe atamaliza kupereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zamgwirizano.
-