-
Numeri 19:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ngati munthu wafera mutenti, lamulo lake ndi ili: Munthu aliyense amene walowa mutentimo komanso aliyense amene anali mutenti momwemo, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.
-
-
Numeri 19:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Aliyense amene wakhudza munthu amene waphedwa ndi lupanga kunja kwa msasa, kapena mtembo, fupa la munthu, kapenanso manda, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.+
-