-
Deuteronomo 20:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mʼmalomwake, mudzawononge anthu onse. Mudzawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani.
-