-
Deuteronomo 18:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma munganene mumtima mwanu kuti: “Tidzadziwa bwanji kuti si Yehova amene walankhula mawuwo?” 22 Mneneri akalankhula mʼdzina la Yehova, koma zimene walankhulazo osachitika kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo. Mneneriyo walankhula mawu amenewo modzikuza ndipo musachite naye mantha.’”
-