6 Mudzachite izi: Iweyo Kora ndi anthu onse amene akukutsatira+ mudzatenge zofukizira.+ 7 Mʼzofukizirazo mudzaikemo moto komanso zofukiza nʼkubwera nazo pamaso pa Yehova mawa. Munthu amene Yehova adzamusankhe,+ ndi amene ali woyera. Inu ana a Levi+ mwawonjeza kwambiri.”