Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 11:31, 32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Zamoyo zimenezi, zomwe zimapezeka zambiri, ndi zodetsedwa kwa inu.+ Aliyense wozikhudza zitafa adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+

      32 Ndiye chilichonse cha zamoyo zimenezi chikafa nʼkugwera pa chinthu china chilichonse, chinthucho chidzakhala chodetsedwa, kaya ndi chiwiya chamtengo, chovala, chikopa kapena chiguduli. Chiwiya chilichonse chimene chimagwiritsidwa ntchito chiziviikidwa mʼmadzi, ndipo chizikhala chodetsedwa mpaka madzulo, kenako chidzakhala choyera.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani