-
Numeri 26:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Amuna onse amene anawerengedwa pakati pa Aisiraeli ndi amenewa ndipo onse pamodzi analipo 601,730.+
-
-
Numeri 26:64Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
64 Koma pakati pa anthu amenewa, panalibe munthu aliyense amene anali mʼgulu la anthu omwe anawerengedwa mʼchipululu cha Sinai, nthawi imene Mose ndi wansembe Aroni anawerenga Aisiraeli.+
-