-
Deuteronomo 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 mʼdziko limene simudzasowa chakudya komanso simudzasowa chilichonse, dziko limene miyala yake amapangira zitsulo, limenenso mʼmapiri ake mudzakumbamo kopa.*
-