Salimo 106:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iwo anamukwiyitsanso pa madzi a ku Meriba,*Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+
32 Iwo anamukwiyitsanso pa madzi a ku Meriba,*Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+