Deuteronomo 28:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yehova adzakubalalitsirani pakati pa mitundu yonse, kuchokera kumalekezero a dziko mpaka kumalekezero ena a dziko.+ Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo komanso milungu yamwala, imene inuyo kapena makolo anu sanaidziwe.+ Nehemiya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chonde, kumbukirani mawu amene munauza* mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+
64 Yehova adzakubalalitsirani pakati pa mitundu yonse, kuchokera kumalekezero a dziko mpaka kumalekezero ena a dziko.+ Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo komanso milungu yamwala, imene inuyo kapena makolo anu sanaidziwe.+
8 Chonde, kumbukirani mawu amene munauza* mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+