Deuteronomo 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni,* (kuphatikizapo mzinda umene uli mʼchigwacho), mpaka kukafika ku Giliyadi, panalibe mzinda umene sitinathe kuugonjetsa. Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.+ Deuteronomo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo tinatenga dzikoli kukhala lathu kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼchigwa cha Arinoni* ndi hafu ya dera lamapiri la Giliyadi. Ndipo ndinapereka mizinda yake kwa fuko la Rubeni ndi fuko la Gadi.+
36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni,* (kuphatikizapo mzinda umene uli mʼchigwacho), mpaka kukafika ku Giliyadi, panalibe mzinda umene sitinathe kuugonjetsa. Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.+
12 Pa nthawi imeneyo tinatenga dzikoli kukhala lathu kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼchigwa cha Arinoni* ndi hafu ya dera lamapiri la Giliyadi. Ndipo ndinapereka mizinda yake kwa fuko la Rubeni ndi fuko la Gadi.+