-
Deuteronomo 4:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Muzisunga malangizo ndi malamulo ake amene ndikukulamulani lero kuti zikuyendereni bwino, inuyo ndi ana anu obwera pambuyo panu, kuti mukhale kwa nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.”+
-