-
Deuteronomo 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu nʼkutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchenjezani lero kuti anthu inu mudzatha ndithu.+
-