-
Deuteronomo 27:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 “Mukawoloka Yorodano, mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Gerizimu+ nʼkudalitsa anthu: Fuko la Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara, Yosefe ndi Benjamini. 13 Ndipo mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Ebala+ kuti azidzavomereza matemberero akamadzatchulidwa: Fuko la Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali.
-