-
Deuteronomo 18:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ngati mneneri wina angadzikuze nʼkulankhula mʼdzina langa mawu amene sindinamulamule kuti alankhule, kapena kulankhula mʼdzina la milungu ina, mneneri ameneyo afe ndithu.+
-