Deuteronomo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muzimupatsa mowolowa manja zimene akufunazo,+ ndipo musamamupatse* zinthuzo monyinyirika. Mukamachita zimenezi, Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita ndi ntchito zanu zonse.+ Salimo 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Miyambo 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Malaki 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Luka 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
10 Muzimupatsa mowolowa manja zimene akufunazo,+ ndipo musamamupatse* zinthuzo monyinyirika. Mukamachita zimenezi, Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita ndi ntchito zanu zonse.+