Numeri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Mose anatumiza anthu kuchokera ku Kadesi kupita kwa mfumu ya Edomu+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene takumana nawo. Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
14 Kenako Mose anatumiza anthu kuchokera ku Kadesi kupita kwa mfumu ya Edomu+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene takumana nawo.