-
Numeri 20:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma mfumu ya Edomu inawayankha kuti: “Musadzere mʼdziko lathu. Mukadzera, ndibwera ndi lupanga kudzamenyana nanu.” 19 Aisiraeliwo anayankha kuti: “Ife tidzangodutsa mumsewu waukulu, ndipo ngati ifeyo kapena ziweto zathu tingamwe madzi anu, tidzakulipirani.+ Sitikufuna chilichonse ayi, koma kungodutsa mʼdziko lanu basi.”+
-