-
Numeri 35:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
-
-
Deuteronomo 27:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 ‘Wotembereredwa ndi munthu wobisalira mnzake nʼkumupha.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
-