Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha. Deuteronomo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha.