Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 21:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ndipo aziuza akulu amzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamva komanso ndi wopanduka ndipo amakana kutimvera. Ndi wosusuka+ komanso ndi chidakwa.’+ 21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+

  • Deuteronomo 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthu akapezeka ataba mmodzi mwa abale ake, Aisiraeli, ndipo wamuchitira nkhanza nʼkumugulitsa,+ wakuba munthuyo ayenera kufa.+ Muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • 1 Akorinto 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani