-
Yoswa 11:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Aisiraeliwo anapha ndi lupanga munthu aliyense amene anali mumzindawo. Panalibe chamoyo chilichonse chimene chinatsala,+ ndipo Yoswa anatentha mzinda wa Hazori.
-